Pang'ono pang'ono
Pang'ono pang'ono
Puma mwananga
Khala apa mwananga
Tsitsa mtima pansi
Puma mwananga
Usaope Dekha
Wafika pakhomo
Puma mwananga
This poem has not been translated into any other language yet.
I would like to translate this poem